Ekisodo 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita mʼtsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.* Anthu onse amene anawerengedwa analipo 603,550.+ Numeri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iweyo ndi Aroni muwalembe mʼkaundula mogwirizana ndi magulu awo.* Uwerenge onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ amene ali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli. Numeri 26:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mliri uja utatha,+ Yehova anauza Mose ndi Eleazara mwana wa wansembe Aroni kuti: 2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+
26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita mʼtsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.* Anthu onse amene anawerengedwa analipo 603,550.+
3 Iweyo ndi Aroni muwalembe mʼkaundula mogwirizana ndi magulu awo.* Uwerenge onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ amene ali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli.
26 Mliri uja utatha,+ Yehova anauza Mose ndi Eleazara mwana wa wansembe Aroni kuti: 2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+