Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+

  • Aroma 8:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo?

  • Tito 2:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 pamene tikuyembekezera zinthu zosangalatsa+ ndiponso kuonekera kwaulemerero kwa Mulungu wamkulu komanso kwa Mpulumutsi wathu, Yesu Khristu, 14 amene anadzipereka mʼmalo mwa ife+ kuti atilanditse*+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse, kuti tikhale anthu ake apadera, odzipereka pa ntchito zabwino.+

  • 1 Yohane 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komatu ngati tikuyenda mʼkuwala mofanana ndi mmenenso iye alili mʼkuwala, ndiye kuti ndife ogwirizana ndipo magazi a Yesu, yemwe ndi Mwana wake, akutiyeretsa ku machimo onse.+

  • 1 Yohane 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tadziwa chikondi chifukwa chakuti Yesu Khristu anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena