Aefeso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndife ntchito ya manja a Mulungu. Iye ndi amene anatilenga+ ndipo ndife ogwirizana ndi Khristu Yesu+ kuti tichite ntchito zabwino, zimene Mulungu anakonzeratu kuti tiyendemo. Aheberi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuli bwanji magazi a Khristu,+ amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu woyera?* Kodi magazi amenewo sadzayeretsa zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika kwa Mulungu wamoyo?+
10 Ndife ntchito ya manja a Mulungu. Iye ndi amene anatilenga+ ndipo ndife ogwirizana ndi Khristu Yesu+ kuti tichite ntchito zabwino, zimene Mulungu anakonzeratu kuti tiyendemo.
14 kuli bwanji magazi a Khristu,+ amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu woyera?* Kodi magazi amenewo sadzayeretsa zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika kwa Mulungu wamoyo?+