Ekisodo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aroni mʼbale wako umupangire zovala zopatulika kuti zimupatse ulemerero ndi kumʼkongoletsa.+ Ekisodo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zovala zopatulika+ za Aroni zidzagwiritsidwa ntchito ndi ana ake+ obwera mʼmbuyo mwake akadzawadzoza nʼkuwaika kuti akhale ansembe. Levitiko 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azivala mkanjo wopatulika wansalu,+ kabudula wansalu+ wobisa* thupi lake, azimanga lamba wansalu wapamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+
29 Zovala zopatulika+ za Aroni zidzagwiritsidwa ntchito ndi ana ake+ obwera mʼmbuyo mwake akadzawadzoza nʼkuwaika kuti akhale ansembe.
4 Azivala mkanjo wopatulika wansalu,+ kabudula wansalu+ wobisa* thupi lake, azimanga lamba wansalu wapamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+