Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uwerenge+ gulu lonse la Aisiraeli* mogwirizana ndi mabanja awo, potengera nyumba za makolo awo, nʼkulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.

  • Deuteronomo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+

  • 1 Akorinto 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere nawo ndipo anaphedwa mʼchipululu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena