Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ana anu adzakhala abusa mʼchipululu kwa zaka 40,+ ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika kwanu,* mpaka womalizira kufa wa inu atagona mʼmanda mʼchipululu muno.+

  • Numeri 32:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, sadzaliona dziko+ limene ndinalumbira kuti ndidzapereka kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.

  • Deuteronomo 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a mʼbadwo woipa uwu amene adzaone dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+

  • Salimo 95:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti:

      “Sadzalowa mumpumulo wanga.”+

  • Aheberi 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nanga kodi analumbirira ndani kuti sadzalowa mumpumulo wake? Kodi si omwe aja amene sanamumvere?

  • Yuda 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zonsezi, ndikufuna kukukumbutsani kuti Yehova* atapulumutsa anthu ake powatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena