Numeri 4:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anawerenga kuyambira azaka 30 mpaka 50, ndipo onse anasankhidwa kuti azitumikira komanso kunyamula katundu wa pachihema chokumanako.+ Numeri 8:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma akakwanitsa zaka 50, azituluka mʼgululo ndipo asamatumikirenso. 26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+
47 Anawerenga kuyambira azaka 30 mpaka 50, ndipo onse anasankhidwa kuti azitumikira komanso kunyamula katundu wa pachihema chokumanako.+
25 Koma akakwanitsa zaka 50, azituluka mʼgululo ndipo asamatumikirenso. 26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+