Numeri 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai. Numeri 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pomaliza, gulu la mafuko atatu la ana a Dani linanyamuka potengera magulu awo.* Iwo ndi amene ankalondera kumbuyo kwa magulu onse a mafukowo. Mtsogoleri wa gululi anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
25 Pomaliza, gulu la mafuko atatu la ana a Dani linanyamuka potengera magulu awo.* Iwo ndi amene ankalondera kumbuyo kwa magulu onse a mafukowo. Mtsogoleri wa gululi anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.