Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo.

      Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu.

  • Numeri 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mabanja a Agerisoni ankamanga misasa yawo kumbuyo kwa chihema,+ mbali yakumadzulo.

  • Numeri 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mabanja a ana a Kohati ankamanga msasa wawo kumʼmwera kwa chihema.+

  • Numeri 3:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga msasa wawo kumpoto kwa chihema.+

  • Numeri 3:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Amene ankamanga msasa wawo kumʼmawa kwa chihema, kumbali yotulukira dzuwa, anali Mose ndi Aroni, ndiponso ana a Aroni. Ntchito yawo inali kutumikira mʼmalo opatulika, mʼmalo mwa Aisiraeli. Munthu wamba aliyense* amene wayandikira malowo, ankayenera kuphedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena