Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 12:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kumunena Mose chifukwa cha mkazi wa Chikusi+ amene anamukwatira. 2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera mwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera mwa ife?”+ Koma Yehova ankamvetsera.+

  • Numeri 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Aisiraeli onse anayamba kungʼungʼudzira Mose ndi Aroni,+ ndipo gulu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera mʼchipululu muno.

  • Salimo 106:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mumsasa, iwo anayamba kuchitira nsanje Mose

      Ndiponso Aroni,+ woyera wa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena