17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu.
9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi. Musamawaopseze chifukwa mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo, ali kumwamba+ ndipo alibe tsankho.