Deuteronomo 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiye ine ndinakuuzani kuti, ‘Musachite mantha kapena kuwaopa.+ Deuteronomo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+ Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani? Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’
6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+
27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?
10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’