-
Numeri 34:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+
3 Malire a dziko lanu mbali yakumʼmwera adzayambire kuchipululu cha Zini, malire ndi Edomu. Malire anu akumʼmwera, mbali yakumʼmawa, adzayambire kumene Nyanja Yamchere* yathera.+
-