Numeri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli, uwauze kuti, ‘Pamene mukukalowa m’dziko la Kanani,+ nawa malire a dziko+ limene mudzalandire ngati cholowa chanu.+
2 “Lamula ana a Isiraeli, uwauze kuti, ‘Pamene mukukalowa m’dziko la Kanani,+ nawa malire a dziko+ limene mudzalandire ngati cholowa chanu.+