Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova akawapatsa woweruza,+ Yehova ankakhala ndi woweruzayo, ndipo ankawapulumutsa mʼmanja mwa adani awo pa nthawi yonse ya woweruzayo. Yehova ankawamvera chisoni+ akamva kulira kwawo chifukwa cha anthu omwe ankawapondereza+ komanso kuwachitira nkhanza.

  • Salimo 107:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iwo ankaitana Yehova kuti awathandize mʼmasautso awo.

      Ndipo iye ankawapulumutsa ku mavuto awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena