-
Oweruza 9:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Zimenezi zinachitika kuti anthu amene anali ndi mlandu wa magazi abwezeredwe nkhanza zimene anachitira ana aamuna 70 a Yerubaala. Zinachitikanso kuti Abimeleki alangidwe chifukwa chopha azichimwene ake+ ndiponso kuti atsogoleri a ku Sekemu alangidwe chifukwa chothandiza Abimeleki kuti aphe azichimwene akewo.
-