Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, musakaphunzire kuchita zinthu zonyansa zimene anthu a mitundu yakumeneko akuchita.+ 10 Pakati panu pasapezeke munthu wowotcha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ aliyense wochita zamatsenga,+ aliyense woombeza,+ wanyanga,+

  • Yesaya 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Inu mwasiya anthu anu, nyumba ya Yakobo,+

      Chifukwa iwo ayamba kutsatira miyambo yambiri ya Kumʼmawa.

      Akuchita zamatsenga+ ngati Afilisiti

      Ndiponso ali ndi ana ambiri a alendo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena