Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,

      Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+

       2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+

      Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+

  • Yakobo 4:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tamverani inu amene mumanena kuti: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko nʼkupeza phindu.”+ 14 Mumanena zimenezi chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Chifukwa muli ngati nkhungu imene imangooneka kwa kanthawi kochepa kenako nʼkuzimiririka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena