Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mʼchaka chachiwiri kuchokera pamene anabwera kunyumba ya Mulungu woona ku Yerusalemu, mʼmwezi wachiwiri, Zerubabele mwana wa Salatiyeli, Yesuwa mwana wa Yehozadaki, abale awo onse, ansembe ndi Alevi ndiponso anthu ena onse amene anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku ukapolo,+ anayamba kugwira ntchito. Anasankha Alevi oyambira zaka 20 kupita mʼtsogolo kuti akhale oyangʼanira ntchito yapanyumba ya Yehova.

  • Ezara 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyi ndi pamene Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli ndi Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki anayamba kumanganso nyumba ya Mulungu+ yomwe inali ku Yerusalemu. Aneneri a Mulungu anali nawo limodzi ndipo ankawathandiza.+

  • Hagai 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndiponso anthu ena onse. Ndipo iwo anabwera nʼkuyamba kugwira ntchito panyumba ya Mulungu wawo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+

  • Zekariya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Satana+ anali ataima kudzanja lamanja la Yoswa kuti azimutsutsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena