Ekisodo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku loyamba muzidzachita msonkhano wopatulika, ndipo pa tsiku la 7 muzidzachitanso msonkhano wina wopatulika. Masiku amenewa musamadzagwire ntchito.+ Koma chakudya choti munthu aliyense adye, chimenecho chokha muzidzaphika. Numeri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.+ Tsiku limeneli lizikhala tsiku loliza lipenga.+ Numeri 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Muzichita chikondwerero posonyeza kulemekeza Yehova masiku 7.+
16 Pa tsiku loyamba muzidzachita msonkhano wopatulika, ndipo pa tsiku la 7 muzidzachitanso msonkhano wina wopatulika. Masiku amenewa musamadzagwire ntchito.+ Koma chakudya choti munthu aliyense adye, chimenecho chokha muzidzaphika.
29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.+ Tsiku limeneli lizikhala tsiku loliza lipenga.+
12 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Muzichita chikondwerero posonyeza kulemekeza Yehova masiku 7.+