Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 75:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mʼdzanja la Yehova muli kapu.+

      Vinyo akuchita thovu ndipo wasakanizidwa bwino.

      Ndithudi, iye adzakhuthula vinyo yense

      Ndipo anthu onse oipa padziko lapansi adzamwa mpaka kugugudiza nsenga zake.”+

  • Yesaya 51:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+

      Iwe amene wamwa zinthu zamʼkapu ya mkwiyo wa Yehova kuchokera mʼdzanja lake.

      Iweyo wamwa zimene zili mʼchipanda,

      Wagugudiza kapu yochititsa kuti munthu aziyenda dzandidzandi.+

  • Yeremiya 25:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Tenga kapu iyi ya vinyo wa mkwiyo imene ili mʼdzanja langa ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.

  • Chivumbulutso 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo wa Mulungu amene akuthiridwa mʼkapu ya mkwiyo wake.+ Ndipo adzazunzidwa ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera komanso pamaso pa Mwanawankhosa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena