Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma inu mumaona mavuto ndi masautso. Mumayangʼana nʼkuchitapo kanthu.+ Munthu wovutika amayangʼana kwa inu,+ Mumathandiza mwana wamasiye.+ Salimo 140:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikudziwa kuti Yehova adzateteza anthu onyozeka pa mlandu wawoNdipo adzachitira chilungamo anthu osauka.+ Miyambo 22:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+23 Chifukwa Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+Ndipo adzachotsa moyo wa anthu amene akuwabera mwachinyengo.
14 Koma inu mumaona mavuto ndi masautso. Mumayangʼana nʼkuchitapo kanthu.+ Munthu wovutika amayangʼana kwa inu,+ Mumathandiza mwana wamasiye.+
12 Ndikudziwa kuti Yehova adzateteza anthu onyozeka pa mlandu wawoNdipo adzachitira chilungamo anthu osauka.+
22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+23 Chifukwa Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+Ndipo adzachotsa moyo wa anthu amene akuwabera mwachinyengo.