Salimo 72:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Litamandike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+ Ame! Ame! Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu kulandira ulemerero,+ ulemu+ ndi mphamvu+ chifukwa munalenga zinthu zonse+ ndipo mwa kufuna kwanu, zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”
19 Litamandike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+ Ame! Ame!
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu kulandira ulemerero,+ ulemu+ ndi mphamvu+ chifukwa munalenga zinthu zonse+ ndipo mwa kufuna kwanu, zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”