Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+ Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale. Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni* pogwiritsa ntchito choonadi.+ Mawu anu ndi choonadi.+
6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale.