Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.* Yeremiya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+ Ezekieli 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+ 1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Poyamba munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa mʼbusa wanu+ ndi woyangʼanira miyoyo yanu.
80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.*
3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+
12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+
25 Poyamba munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa mʼbusa wanu+ ndi woyangʼanira miyoyo yanu.