Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mdaniyo anati: ‘Ndiwathamangira nʼkuwapeza!

      Ndigawa chuma chawo mpaka nditakhutira!

      Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+

      10 Mwapemerera mpweya wanu, ndipo nyanja yawamiza.+

      Amira mʼmadzi akuya ngati chitsulo cholemera.

  • Luka 12:18-20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno anati, ‘Ndichita izi:+ Ndigwetsa nyumba zanga zosungiramo zinthu nʼkumanga zikuluzikulu, ndipo tirigu wanga yense ndi zinthu zanga zonse ndidzazitutira mmenemo, 19 ndiye ndidzadziuza kuti: “Uli ndi zinthu zambiri zabwino ndipo zisungika kwa zaka zambiri. Mtima mʼmalo, udye, umwe ndi kusangalala.”’ 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena