Machitidwe 10:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+ Chivumbulutso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+
34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+
10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+