Ezekieli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzaumitsa ngalande zamumtsinje wa Nailo+ ndipo ndidzagulitsa dzikolo kwa anthu oipa. Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu ochokera kudziko lina.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’ Zekariya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.Ndidzamenya mafunde a nyanjayo,+Ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma. Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa,Ndipo ndodo yachifumu ya Iguputo idzachoka.+
12 Ndidzaumitsa ngalande zamumtsinje wa Nailo+ ndipo ndidzagulitsa dzikolo kwa anthu oipa. Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu ochokera kudziko lina.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’
11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.Ndidzamenya mafunde a nyanjayo,+Ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma. Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa,Ndipo ndodo yachifumu ya Iguputo idzachoka.+