Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri. Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku limenelo Aiguputo adzakhala ngati akazi ndipo adzanjenjemera ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzatambasula dzanja loopsa kuti awapatse chilango.+
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri.
16 Pa tsiku limenelo Aiguputo adzakhala ngati akazi ndipo adzanjenjemera ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzatambasula dzanja loopsa kuti awapatse chilango.+