Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+

      Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+

      Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo.

      Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+

  • Ezekieli 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzakusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu ndipo udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Mzinda wako sudzamangidwanso chifukwa ine Yehova ndanena,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Ezekieli 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati:

      “Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi!+ Mwa iwe munkakhala anthu ochokera kunyanja.

      Iwe ndi anthu ako munali amphamvu panyanja,+

      Munkachititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena