2 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anapitiriza kuwatumizira aneneri kuti awathandize kubwerera kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kuwachenjeza, koma sanamvere.+ Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Zekariya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve.+
19 Yehova anapitiriza kuwatumizira aneneri kuti awathandize kubwerera kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kuwachenjeza, koma sanamvere.+
26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve.+