Deuteronomo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Auze anthuwo kuti: “Mudutsa mʼmalire a dziko la abale anu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.
4 Auze anthuwo kuti: “Mudutsa mʼmalire a dziko la abale anu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.