Deuteronomo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Auze anthuwo kuti: “Mukudutsa m’malire a dziko la abale anu,+ ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.
4 Auze anthuwo kuti: “Mukudutsa m’malire a dziko la abale anu,+ ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.