Machitidwe 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Ankalowa mʼnyumba iliyonse nʼkumakokera panja amuna ndi akazi omwe, ndipo ankawapititsa kundende.+ Agalatiya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munamva ndithu zimene ndinkachita ndili mʼChiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri mpingo wa Mulungu ndipo ndinapitiriza kuuwononga.+ Agalatiya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene kale ankatizunza uja+ komanso kuwononga mipingo* tsopano akulengeza uthenga wabwino.”+
3 Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Ankalowa mʼnyumba iliyonse nʼkumakokera panja amuna ndi akazi omwe, ndipo ankawapititsa kundende.+
13 Munamva ndithu zimene ndinkachita ndili mʼChiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri mpingo wa Mulungu ndipo ndinapitiriza kuuwononga.+
23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene kale ankatizunza uja+ komanso kuwononga mipingo* tsopano akulengeza uthenga wabwino.”+