Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Popeza ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwirira ntchito limodzi,+ chifukwa onse anali opanga matenti.

  • 1 Akorinto 4:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mpaka pano tikadali anjala,+ aludzu+ ndiponso ausiwa. Tikumenyedwabe,+ tikusowabe pokhala 12 ndipo tikugwirabe ntchito mwakhama ndi manja athu.+ Akamatinenera zachipongwe, timadalitsa+ ndipo akamatizunza, timapirira moleza mtima.+

  • 1 Atesalonika 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndithudi abale, mukukumbukira kuti tinayesetsa kugwira ntchito mwakhama ndi mphamvu zathu zonse. Tinkagwira ntchito usiku ndi masana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza,+ pamene tinkalalikira uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena