1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, ngati mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ Afilipi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani. 1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munalandira mawuwo ndi chimwemwe chimene mzimu woyera+ umapereka ngakhale kuti munali pamavuto aakulu. Pamenepa munatsanzira ifeyo+ komanso munatsanzira Ambuye,+
17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.
6 Munalandira mawuwo ndi chimwemwe chimene mzimu woyera+ umapereka ngakhale kuti munali pamavuto aakulu. Pamenepa munatsanzira ifeyo+ komanso munatsanzira Ambuye,+