2 Akorinto 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+ 2 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ngati achisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri komanso ngati opanda chilichonse koma okhala ndi zinthu zonse.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse muzisangalala chifukwa cha Ambuye. Ndikubwerezanso kunena kuti, Muzisangalala!+
4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+
10 ngati achisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri komanso ngati opanda chilichonse koma okhala ndi zinthu zonse.+