Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho, kodi pamenepa palinso chifukwa chodzitamira? Palibetu. Kodi tizidzitama chifukwa chotsatira Chilamulo?+ Ndithudi ayi, koma chifukwa chotsatira lamulo la chikhulupiriro.

  • 1 Akorinto 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kwa anthu amene sayendera Chilamulo ndinakhala ngati wosayendera Chilamulo, kuti ndithandize anthu osayendera Chilamulo. Ndinachita zimenezi ngakhale kuti ndimatsatira malamulo a Mulungu komanso lamulo la Khristu.+

  • Agalatiya 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pitirizani kunyamulirana zinthu zolemera.+ Mukamachita zimenezi mudzakhala mukukwaniritsa chilamulo cha Khristu.+

  • Akolose 2:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuwonjezera pamenepo, ngakhale kuti munali akufa chifukwa cha machimo anu komanso chifukwa choti munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu.+ Mokoma mtima anatikhululukira machimo athu onse+ 14 ndipo anafafaniza Chilamulo+ chimene chinali ndi malamulo ambirimbiri+ omwe ankatitsutsa.+ Iye anachichotsa pochikhomerera pamtengo wozunzikirapo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena