Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza mpaka liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ Deuteronomo 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo andikwiyitsa* ndi milungu yabodza.+Andikhumudwitsa ndi mafano awo opanda pake.+ Choncho ine ndiwachititsa nsanje ndi anthu opanda pake,+Ndiwakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza mpaka liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+
21 Iwo andikwiyitsa* ndi milungu yabodza.+Andikhumudwitsa ndi mafano awo opanda pake.+ Choncho ine ndiwachititsa nsanje ndi anthu opanda pake,+Ndiwakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+