Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 61:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzasangalala kwambiri mwa Yehova.

      Ndidzasangalala mwa Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.+

      Chifukwa iye wandiveka zovala zachipulumutso.+

      Wandiveka mkanjo wa chilungamo,*

      Ngati mkwati amene wavala nduwira yofanana ndi ya wansembe,+

      Ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.

  • Aefeso 5:25-27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Amuna inu, pitirizani kukonda akazi anu+ ngati mmenenso Khristu anakondera mpingo nʼkudzipereka yekha chifukwa cha mpingowo,+ 26 nʼcholinga choti auyeretse pousambitsa mʼmadzi a mawu a Mulungu.+ 27 Anachita zimenezi kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero, wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zoterezi,+ koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+

  • Chivumbulutso 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Amenewa ndi amene sanadzidetse ndi akazi ndipo ali ngati anamwali.+ Iwo ndi amene amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ pakati pa anthu ngati zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena