-
Chivumbulutso 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma chilombocho chinagwidwa limodzi ndi mneneri wabodza+ uja, amene anachita zizindikiro pamaso pa chilombocho. Zizindikiro zimenezi anasocheretsa nazo amene analandira chizindikiro cha chilombo+ komanso amene ankalambira chifaniziro chake.+ Onse awiri adakali amoyo, anaponyedwa mʼnyanja ya moto yoyaka ndi sulufule.+
-