Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Atesalonika 1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Atesalonika

      • Moni (1)

      • Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Atesalonika (2-10)

1 Atesalonika 1:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Amene ankadziwikanso kuti Sila.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:22; 1Pe 5:12
  • +Mac 16:1, 2

1 Atesalonika 1:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 1:11, 12

1 Atesalonika 1:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 1:3, 4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2007, ptsa. 6-7

    Utumiki wa Ufumu,

    2/2000, tsa. 4

1 Atesalonika 1:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Sukulu ya Utumiki, tsa. 194

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2000, ptsa. 16-17

    Utumiki wa Ufumu,

    2/2000, ptsa. 3-4

1 Atesalonika 1:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 2:14
  • +1Ak 11:1; Afi 3:17; 2At 3:9
  • +1Pe 2:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki wa Ufumu,

    2/2000, ptsa. 3-4

1 Atesalonika 1:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 1:4

1 Atesalonika 1:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 10:14; 12:2; Aga 4:8; 1Yo 5:21

1 Atesalonika 1:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 1:10, 11; Tit 2:13
  • +1At 5:2; 2Pe 3:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2010, tsa. 13

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Ates. 1:1Mac 15:22; 1Pe 5:12
1 Ates. 1:1Mac 16:1, 2
1 Ates. 1:22At 1:11, 12
1 Ates. 1:31Pe 1:3, 4
1 Ates. 1:61At 2:14
1 Ates. 1:61Ak 11:1; Afi 3:17; 2At 3:9
1 Ates. 1:61Pe 2:21
1 Ates. 1:82At 1:4
1 Ates. 1:91Ak 10:14; 12:2; Aga 4:8; 1Yo 5:21
1 Ates. 1:101At 5:2; 2Pe 3:12
1 Ates. 1:10Mac 1:10, 11; Tit 2:13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Atesalonika 1:1-10

Kalata Yoyamba Yopita kwa Atesalonika

1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano*+ komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate komanso Ambuye Yesu Khristu kuti:

Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zikhale nanu.

2 Nthawi zonse timathokoza Mulungu tikamakutchulani nonsenu mʼmapemphero athu.+ 3 Timachita zimenezi chifukwa nthawi zonse timakumbukira ntchito zanu zachikhulupiriro, ntchito zanu zachikondi komanso kupirira kwanu chifukwa cha chiyembekezo chimene muli nacho+ mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu amene ndi Atate wathu. 4 Chifukwa tikudziwa, inu abale okondedwa ndi Mulungu, kuti iye ndi amene anakusankhani. 5 Tikutero chifukwa pamene tinkalalikira uthenga wabwino kwa inu, sitinkangolankhula basi, koma uthengawo unali wamphamvu, unabwera ndi mzimu woyera komanso tinalalikira motsimikiza mtima kwambiri. Inunso mukudziwa zimene tinakuchitirani pofuna kukuthandizani. 6 Munalandira mawuwo ndi chimwemwe chimene mzimu woyera+ umapereka ngakhale kuti munali pamavuto aakulu. Pamenepa munatsanzira ifeyo+ komanso munatsanzira Ambuye,+ 7 moti munakhala chitsanzo kwa okhulupirira onse ku Makedoniya ndi ku Akaya.

8 Sikuti mawu a Yehova* ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha, koma kwina kulikonse chikhulupiriro chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu. 9 Chifukwa iwo akunenabe za mmene ife tinakumanirana ndi inu koyamba komanso mmene inu munasiyira mafano anu nʼkutembenukira kwa Mulungu,+ kuti muzitumikira Mulungu wamoyo ndi woona. 10 Munatembenukiranso kwa Mulungu kuti muziyembekezera Mwana wake kuchokera kumwamba,+ amene anamuukitsa kwa akufa. Mwanayo ndi Yesu, amene akutipulumutsa ku mkwiyo umene ukubwerawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena