1 AKORINTO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Mawu oyamba (1-3)
Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha Akorinto (4-9)
Anawalangiza kuti akhale ogwirizana (10-17)
Khristu ndi mphamvu komanso nzeru ya Mulungu (18-25)
Kudzitama mwa Yehova (26-31)
2
Paulo analalikira ku Korinto (1-5)
Nzeru za Mulungu ndi zapamwamba (6-10)
Kusiyana pakati pa munthu wauzimu ndi munthu wokonda za mʼdziko (11-16)
3
Akorinto ankakondabe zinthu za mʼdziko (1-4)
Mulungu ndi amene amakulitsa (5-9)
Kumanga ndi zinthu zosagwira moto (10-15)
Ndinu kachisi wa Mulungu (16, 17)
Nzeru zamʼdziko ndi zopusa kwa Mulungu (18-23)
4
Atumiki ayenera kukhala okhulupirika (1-5)
Atumiki a Chikhristu ayenera kukhala odzichepetsa (6-13)
Paulo ankasamalira ana ake auzimu (14-21)
5
Nkhani ya munthu yemwe anachita chiwerewere (1-5)
Zofufumitsa zochepa zimafufumitsa mtanda wonse (6-8)
Munthu woipa anayenera kuchotsedwa (9-13)
6
Akhristu ankatengerana kukhoti (1-8)
Anthu amene sadzalowa mu Ufumu (9-11)
Lemekezani Mulungu ndi matupi anu (12-20)
7
Malangizo a anthu amene sali pabanja ndi amene ali pabanja (1-16)
Mukhale mmene munalili pamene munkaitanidwa (17-24)
Anthu omwe sali pabanja ndiponso akazi amasiye (25-40)
8
9
10
Zitsanzo zotichenjeza za Aisiraeli (1-13)
Chenjezo pa nkhani yolambira mafano (14-22)
Ufulu ndiponso kuganizira ena (23-33)
11
12
13
14
15
Kuukitsidwa kwa Khristu (1-11)
Kuuka kwa akufa ndi maziko a chikhulupiriro (12-19)
Kuuka kwa Khristu kumatitsimikizira kuti akufa adzauka (20-34)
Thupi la mnofu ndiponso thupi lauzimu (35-49)
Thupi loti silingafe kapena kuwonongeka (50-57)
Kuchita zambiri pa ntchito ya Ambuye (58)
16
Kutolera zopereka zopita kwa Akhristu a ku Yerusalemu (1-4)
Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (5-9)
Ulendo wa Timoteyo ndiponso wa Apolo (10-12)
Malangizo ndiponso kupereka moni (13-24)