AROMA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Mawu oyamba (1-7)
Paulo ankafunitsitsa kupita ku Roma (8-15)
Wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro (16, 17)
Anthu alibe chifukwa chosakhulupirira kuti kuli Mulungu (18-32)
2
Chiweruzo cha Mulungu kwa Ayuda ndi Agiriki (1-16)
Ayuda ndiponso Chilamulo (17-24)
Mdulidwe wa mumtima (25-29)
3
‘Mulungu amanena zoona’ (1-8)
Ayuda ndi Agiriki omwe ndi ochimwa (9-20)
Kukhala wolungama chifukwa cha chikhulupiriro (21-31)
4
5
Kugwirizananso ndi Mulungu kudzera mwa Khristu (1-11)
Timafa chifukwa cha Adamu, timakhala ndi moyo chifukwa cha Khristu (12-21)
6
Moyo watsopano kudzera mu ubatizo wogwirizana ndi Khristu (1-11)
Musalole kuti uchimo uzilamulira matupi anu (12-14)
Kuchoka ku ukapolo wauchimo nʼkukhala akapolo a Mulungu (15-23)
7
Fanizo losonyeza mmene munthu amamasukira ku Chilamulo (1-6)
Chilamulo chinathandiza kuti uchimo uonekere (7-12)
Kulimbana ndi uchimo (13-25)
8
Mzimu umabweretsa moyo ndi ufulu (1-11)
Mzimu umachitira umboni (12-17)
Chilengedwe chikudikira ufulu wa ana a Mulungu (18-25)
‘Mzimu umachonderera mʼmalo mwathu’ (26, 27)
Mulungu anawasankhiratu (28-30)
Tikugonjetsa zinthu zonse chifukwa cha chikondi cha Mulungu (31-39)
9
Paulo ankamvera chisoni Aisiraeli (1-5)
Mbadwa zenizeni za Abulahamu (6-13)
Palibe angatsutse zimene Mulungu wasankha (14-26)
Anthu ochepa okha ndi amene adzapulumuke (27-29)
Aisiraeli anapunthwa (30-33)
10
11
Si Aisiraeli onse amene anakanidwa (1-16)
Fanizo la mtengo wa maolivi (17-32)
Nzeru za Yehova nʼzozama (33-36)
12
Mupereke matupi anu ngati nsembe ya moyo (1, 2)
Thupi limodzi koma mphatso zosiyanasiyana (3-8)
Malangizo okhudza moyo wa Chikhristu (9-21)
13
Kugonjera olamulira (1-7)
Chikondi chimakwaniritsa Chilamulo (8-10)
Tizichita zinthu ngati masana (11-14)
14
15
Tizilandirana ngati mmene Khristu anatilandirira (1-13)
Paulo, mtumiki wa anthu a mitundu ina (14-21)
Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (22-33)
16
Paulo anauza anthu za Febe yemwe ankatumikira mumpingo (1, 2)
Moni wopita kwa Akhristu a ku Roma (3-16)
Anachenjeza za kugawikana (17-20)
Moni wochokera kwa anzake a Paulo (21-24)
Chinsinsi chopatulika tsopano chadziwika (25-27)