YAKOBO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Moni (1)
Kupirira kumachititsa kuti tikhale osangalala (2-15)
Chikhulupiriro chimakhala cholimba tikamayesedwa (3)
Tizipempha ndi chikhulupiriro (5-8)
Chilakolako chimabweretsa uchimo ndi imfa (14, 15)
Mphatso iliyonse yabwino imachokera kumwamba (16-18)
Kumva ndi kuchita zimene mawu akunena (19-25)
Kulambira koyera komanso kosadetsedwa (26, 27)
2
3
4
5
Anachenjeza anthu achuma (1-6)
Mulungu amadalitsa anthu amene amayembekezera moleza mtima (7-11)
Mukati “ayi,” azikhaladi ayi (12)
Pemphero lachikhulupiriro limagwira ntchito (13-18)
Kuthandiza munthu wochimwa kuti abwerere (19, 20)