Tsamba 2
Kudula Msinga za Kusaphunzira 3-9
Anthu oposa chigawo chimodzi mwa zinayi cha anthu achikulire padziko sangathe kuŵerenga kapena kulemba. Kodi nchifukwa ninji ochuluka motero ali osaphunzira, ndipo nchiyani chimene chingachitidwe kuthetsa vuto la dziko lonse limeneli?
Aaborijini a ku Australia—Anthu Apadera 16
Kodi iwo anachokera kuti? Kodi anali kukhala motani? Kodi ndiziyembekezo zotani zimene ali nazo ponena za mtsogolo?