Tsamba 2
Kodi Chipembedzo Chili ndi Ntchitonso? 3-11
Western Europe achita ngati akutaya chikhulupiriro chake “chachikristu.” Kodi nchifukwa ninji pali mphwayi? Kodi zimenezi ndizo umboni wa mphwayi yofananayo imene idzachitika kumakontinenti ena?
Kodi Akristu Oona Angayembekezere Chitetezero cha Mulungu? 16
Kodi nchifukwa ninji ena amafa akuchita chifuniro cha Mulungu, pamene kuli kwakuti ena amene ali m’mikhalidwe yangozi amakhala ndi moyo?