Tsamba 2
Kodi Muyenera Kulankhulana Ndi Akumalo A Mizimu? 3-10
Anthu kulikonse amayesa kulankhulana ndi akumalo a mizimu. Amafuna- funa chidziŵitso cha mtsogolo. Amafuna chitsogozo pamavuto a moyo wa tsiku ndi tsiku. Kodi kulidi kotheka kulankhulana ndi akumalo a mizimu? Kodi ndani amene amakhalako? Kodi muyenera kuyesa kulankhulana nawo?
Kugonjera kwa Mkazi—Kodi Kumatanthauzanji? 26
Kodi Mawu a Mulungu amanenanji pa kugonjera kwa mkazi kwa mwamuna wake?
[Chithunzi patsamba 2]
Leslie’s