Zisonyezero za Voliyumu 77 ya Galamukani!
ACHICHEPERE AKUFUNSA
Achichepere Ena Amangosangalala Mmene Afunira, 8/8
Alternative Rock, 12/8
Bwenzi Laloŵa m’Vuto, 2/8
Kodi Ndiyenera Kupita ku Makonsati a Rock? 1/8
Fodya Wosasuta—Alibe Ngozi? 5/8
Maseŵero Apakompyuta ndi Apavidiyo, 9/8
Maseŵero a Timu, 3/8, 4/8
Nchifukwa Ninji Mulungu Amalola Zinthu Zoipa Kuchitika? 11/8
Nchifukwa Ninji Sindimakhala ndi Mabwenzi? 6/8
Nchifukwa Ninji Sindimatha Kuphunzira? 7/8
Ndingapeze Motani Nthaŵi ya Kukondwera? 10/8
CHIPEMBEDZO
Chipembedzo Chili ndi Ntchitonso? 4/8
Chipembedzo Chikupita? 11/8
Kulankhulana ndi Akumalo a Mizimu, 12/8
Kuphunzira Baibulo—m’Malo Osonyezerako Zinyama! 3/8
Ulendo wa Papa ku UN, 7/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Kuyendetsa Bwino Ndalama Zanu, 1/8
Ulova, 3/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chilango cha Imfa, 3/8
Chitetezero cha Mulungu, 4/8
Chikondi Chimene Chimamangirira, 10/8
Kuchotsa, 9/8
Kugonjera kwa Mkazi, 12/8
Kuvina, 5/8
Kuwopa Akufa? 8/8
Ma UFO, 7/8
Mariya ndi “Amayi wa Mulungu”? 1/8
Nchitsogozo Chayani Chimene Mungadalire? 11/8
Pamene Mulakwira Ena, 2/8
Zikondwerero za Carnival, 6/8
MAIKO NDI ANTHU
Anthu Okhala pa Nsanja (Benin), 10/8
Eni America, 9/8
“Ukwati wa Mwambo” ku Ghana, 12/8
MAUNANSI A ANTHU
A Mlandu pa Zochita Zathu? 10/8
Kodi Mungadalire Yani?
Kodi Ndani Ayenera Kusankha za Ukulu wa Banja? 10/8
Kuleka Mawu Opweteka ndi Kunena Mawu Olamitsa, 11/8
Kulera Ana a Ena, 5/8
Kuti Ndilankhule ndi Mwana Wanga Ndinaphunzira Chinenero China (Wogontha), 11/8
Kuvuta Akazi, 6/8
Mudzi wa Dziko Lonse Koma Wogaŵanikabe, 7/8
MBONI ZA YEHOVA
Anasintha Zinthu Zake Zoyamba (J. Sorensen), 8/8
Kupita Patsogolo ndi Manja Amene Amapereka Zizindikiro (Misonkhano Yachigawo ya Ogontha), 4/8
Zothandiza Kuwongolera Opaleshoni ya Mtima, 2/8
SAYANSI
Kodi Munaonapo Kuŵalima Kobiliŵira? 6/8
Thambo Lodabwitsa, 2/8
UMOYO NDI MANKHWALA
AIDS mu Afirika—Kodi Dziko Lachikristu Lili ndi Mlandu? 5/8
Gwiritsirani Ntchito Mankhwala Mwanzeru, 10/8
Ndudu za Fodya—Kodi Mumazikana? 11/8
Ntchentche ya Kambalame, 6/8
Nthenda ya Mtima, 12/8
Thanzi ndi Malo Okhala, 3/8
Vairasi Yakupha Isakaza Zaire, 5/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Amgubuduza Tubzi a mu Afirika, 3/8
Kuphunzira Baibulo—M’malo Osonyezerako Zinyama, 3/8
Masamba a Chinangwa, 7/8
Ntchentche Zonyansazo, 4/8
Nyama Zokhala Pangozi, 8/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
“Dongosolo la Dziko Latsopano”—Chiyambi Chosalimba, 8/8
Kodi Boma Lingathetse Upandu? 10/8
Kuipitsa kwa Magalimoto, 6/8
Kupeka Ndalama—Vuto Lapadziko Lonse, 4/8
Kuvuta Akazi—Vuto Lapadziko Lonse, 6/8
Masoka Achilengedwe—Kuthandiza Mwana Kulimbana Nawo, 7/8
Pamene Sikudzakhalanso Nkhondo, 5/8
Pulaneti Lathu Lokhala Pangozi, 1/8
Ufulu wa Kulankhula, 8/8
Vuto la Othaŵa Kwawo, 9/8
ZOSIYANASIYANA
Dzitetezereni ku Mphezi! 3/8
Konzani Mphamvu Yanu ya Kukumbukira, 4/8
Matchuti, 7/8
Peŵani Ulesi wa Kuŵerenga, 2/8
Unamwali—Chifukwa Ninji? 9/8