Tsamba 2
Dziko Lopanda Upandu—Lidzakhalako Liti? 3-9
Anthu Mamiliyoni Lerolino Amakhulupirira Kuti Pakhoza Kukhala Dziko Lopanda Upandu. Kodi Mungadzalione Motani?
Ndinalimbikitsidwa ndi Kukhulupirika kwa Banja Lathu kwa Mulungu 10
Horst akali wachinyamata, atate ake ndi mlongo wake anamwalira m’ndende ku Germany panthaŵi ya Nkhondo Yadziko II Kodi moyo wake unakhudzidwa motani?
Atolankhani a ku Russia Athokoza Mboni za Yehova 22
Ŵerengani zomwe nyuzipepala zinanena za kupatulira kwa ofesi ya nthambi ya ku Russia ya Mboni za Yehova chilimwe chathachi.